Mundikumbuke

3 views

Lyrics

Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
 Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine Mundikumbuke
 Amayo ndatsala ndeka [repeat 4] Amai asanafe anasiya
 Mawu
 Amai asanafe anasiya mawu oooohh Udzafune fune moenda,
 Bambo ulinawo [repeat 4] Ndili mwana wapancili, wokula
 NaAmai
 Ndili mwana wapancili ine, wokula naAmai Ndili wamasiye
 Wokulila muumpawi
 Ndili wamasiye wokulila muumpawi
 Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi
 Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi Azimai ancili ana
 Amasiye mvelani
 Azimai ancili eh ana amasiye Angazopeni monga ana
 Anunso
 Angazopeni monga ana anunso wosataya
 Angazopeni ye monga ana anunso
 Angazopeni ye monga ana anunso Chifundo, ndili chifundo
 Ine
 Chifundo, ndili chifundo ine
 Mavhuto, ndili mavhuto ine
 Mavhuto, ndili mavhuto ine Amai anandilela anamwalila
 Kale
 Amai anandilela ine anamwalila kale Poenda ndimangolila,
 Kukumbuka ondibala
 Poenda ndimangolila ine, kukumbuka ondibala Pogona
 Ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu
 Pogona ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu
 Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu
 Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu Ngati muli
 Ndiumoyo, kapena munamwalila
 Ngati muli ndiumoyo, kapena munamwalila Bwanji
 Osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
 Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko Chifundo,
 Ndili chifundo ine
 Chifundo, ndili chifundo ine
 Mavhuto, ndili mavhuto ine
 Mavhuto, ndili mavhuto ine

Audio Features

Song Details

Duration
08:51
Key
11
Tempo
128 BPM

Share

More Songs by Alick Macheso

Similar Songs