Chautah
3
views
Lyrics
Chauta woo! Tsiku loyamba lomwelija Lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo Ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Chauta woo! Tsiku loyamba lomwelija Lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo Ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Nkhope yanga Ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga Ndikhala ngati ndiliupita or bwera, Silidziwika bwino, i Koma munakanchinja nkhope Nkhope yanga Ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga Ndikhala ngati ndiliupita or bwera, Silidziwika bwino, i Koma munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chauta munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chauta ndaona bvuto
Audio Features
Song Details
- Duration
- 07:13
- Key
- 4
- Tempo
- 131 BPM