Chautah
3
views
Lyrics
Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah ndaona vhuto Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah ndaona vhuto Dendera Kings Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Chautah woo! Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija Limene munali kulenga ine Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera Silidziwika bwino Koma munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah munakanchinja nkhope Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa) Oyang'ana (andiyesa wakuba ine) Oyang'ana (andiyesa wolodza) Chautah ndaona vhuto Dendera Kings Yes! Dendera Kings
Audio Features
Song Details
- Duration
- 07:45
- Key
- 9
- Tempo
- 126 BPM